Mateyu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anthu anamubweretsera ana aangʼono kuti awaike manja nʼkuwapempherera, koma ophunzirawo anawakalipira.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:13 Yesu—Ndi Njira, tsa. 222 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 9
13 Kenako anthu anamubweretsera ana aangʼono kuti awaike manja nʼkuwapempherera, koma ophunzirawo anawakalipira.+