Mateyu 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Yesu anawauza kuti: “Asiyeni anawo ndipo musawaletse kuti abwere kwa ine, chifukwa Ufumu wakumwamba ndi wa anthu ngati amenewa.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 222 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 9
14 Koma Yesu anawauza kuti: “Asiyeni anawo ndipo musawaletse kuti abwere kwa ine, chifukwa Ufumu wakumwamba ndi wa anthu ngati amenewa.”+