Mateyu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano munthu wina anabwera kwa iye nʼkumufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi ndi zinthu zabwino ziti zimene ndikuyenera kuchita kuti ndikapeze moyo wosatha?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:16 Nsanja ya Olonda,6/15/1986, ptsa. 8-9
16 Tsopano munthu wina anabwera kwa iye nʼkumufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi ndi zinthu zabwino ziti zimene ndikuyenera kuchita kuti ndikapeze moyo wosatha?”+