Mateyu 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma ambiri amene ali oyamba adzakhala omaliza ndipo omaliza adzakhala oyamba.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:30 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 225-226 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, ptsa. 8-98/1/1989, tsa. 9