Mateyu 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso musamatchule aliyense kuti atate wanu padziko lapansi pano, chifukwa Atate+ wanu ndi mmodzi Yekhayo, amene amakhala kumwamba. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:9 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 20 Galamukani!,8/8/1992, tsa. 13
9 Komanso musamatchule aliyense kuti atate wanu padziko lapansi pano, chifukwa Atate+ wanu ndi mmodzi Yekhayo, amene amakhala kumwamba.