-
Mateyu 23:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndipo aliyense amene watchula kumwamba polumbira, walumbirira mpando wachifumu wa Mulungu komanso Mulungu amene wakhala pampandowo.
-