Mateyu 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu!+ Chifukwa mumamanga manda a aneneri ndi kukongoletsa manda* a anthu olungama,+
29 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu!+ Chifukwa mumamanga manda a aneneri ndi kukongoletsa manda* a anthu olungama,+