Mateyu 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma kapolo amene analandira imodzi yokha uja anapita kukakumba pansi nʼkubisa ndalama* ya mbuye wakeyo. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:18 Nsanja ya Olonda,8/1/2012, ptsa. 28-29
18 Koma kapolo amene analandira imodzi yokha uja anapita kukakumba pansi nʼkubisa ndalama* ya mbuye wakeyo.