Mateyu 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa mapeto pake kunabwera kapolo amene analandira talente imodzi uja, ndipo anati: ‘Ambuye, ndinkadziwa kuti inu ndinu munthu wovuta. Mumakolola kumene simunafese ndipo mumatuta tirigu kumene simunapete.+
24 Pa mapeto pake kunabwera kapolo amene analandira talente imodzi uja, ndipo anati: ‘Ambuye, ndinkadziwa kuti inu ndinu munthu wovuta. Mumakolola kumene simunafese ndipo mumatuta tirigu kumene simunapete.+