-
Mateyu 26:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Iye anati: “Pitani mumzinda kwa Munthu wakutiwakuti ndipo mukamuuze kuti, ‘Mphunzitsi wanena kuti: “Nthawi yanga yoikidwiratu yayandikira. Ndidzachita phwando la Pasika pamodzi ndi ophunzira anga kunyumba kwako.”’”
-