Mateyu 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma ndikukuuzani kuti: Sindidzamwanso chakumwa chilichonse chochokera ku mphesa ngati ichi mpaka tsiku limene ndidzamwe chatsopano limodzi ndi inu mu Ufumu wa Atate wanga.”+
29 Koma ndikukuuzani kuti: Sindidzamwanso chakumwa chilichonse chochokera ku mphesa ngati ichi mpaka tsiku limene ndidzamwe chatsopano limodzi ndi inu mu Ufumu wa Atate wanga.”+