-
Mateyu 26:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Kenako anabwerera kwa ophunzira aja nʼkuwauza kuti: “Zoona nthawi ngati ino mukugona ndi kupumula? Taonani! Nthawi yoti Mwana wa munthu aperekedwe mʼmanja mwa anthu ochimwa yayandikira.
-