Mateyu 26:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Koma zonsezi zachitika kuti zimene aneneri analemba zikwaniritsidwe.”*+ Kenako ophunzira ake onse anamuthawa nʼkumusiya yekha.+
56 Koma zonsezi zachitika kuti zimene aneneri analemba zikwaniritsidwe.”*+ Kenako ophunzira ake onse anamuthawa nʼkumusiya yekha.+