-
Maliko 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ngakhalenso anthu ambiri ochokera ku Yerusalemu, ku Idumeya, kutsidya la Yorodano komanso ochokera mʼmadera a ku Turo ndi Sidoni, anamva zonse zimene iye ankachita ndipo anapita kwa iye.
-