Maliko 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano pamene anali payekha, ena amene anali naye chapafupi limodzi ndi atumwi 12 aja, anayamba kumufunsa zokhudza mafanizo aja.+
10 Tsopano pamene anali payekha, ena amene anali naye chapafupi limodzi ndi atumwi 12 aja, anayamba kumufunsa zokhudza mafanizo aja.+