Maliko 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anapitiriza kuwauza kuti: “Mvetserani mosamala zimene ndikunenazi.+ Muyezo umene mukuyezera ena, nanunso adzakuyezerani womwewo. Inde, adzakuwonjezerani zochuluka. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 110 Nsanja ya Olonda,4/15/1987, tsa. 8
24 Anapitiriza kuwauza kuti: “Mvetserani mosamala zimene ndikunenazi.+ Muyezo umene mukuyezera ena, nanunso adzakuyezerani womwewo. Inde, adzakuwonjezerani zochuluka.