-
Maliko 4:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Pangʼonopangʼono, payokha nthaka ija imabereka zipatso. Choyamba tirigu amakula, kenako amatulutsa ngala, pamapeto pake maso okhwima a tirigu amaonekera mʼngalamo.
-