Maliko 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atamva zimenezi anadzuka nʼkudzudzula mphepoyo komanso kuuza nyanjayo kuti: “Leka! Khala bata!”+ Atatero mphepoyo inaleka ndipo kenako panachita bata lalikulu. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:39 Nsanja ya Olonda,6/15/2015, tsa. 6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113
39 Atamva zimenezi anadzuka nʼkudzudzula mphepoyo komanso kuuza nyanjayo kuti: “Leka! Khala bata!”+ Atatero mphepoyo inaleka ndipo kenako panachita bata lalikulu.