Maliko 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anamuchonderera mobwerezabwereza kuti: “Mwana wanga wamkazi akudwala mwakayakaya.* Chonde tiyeni mukamuike manja+ kuti achire nʼkukhala ndi moyo.”
23 Iye anamuchonderera mobwerezabwereza kuti: “Mwana wanga wamkazi akudwala mwakayakaya.* Chonde tiyeni mukamuike manja+ kuti achire nʼkukhala ndi moyo.”