-
Maliko 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mzimuwo umati ukamugwira, umamugwetsera pansi. Akatero amachita thovu mʼkamwa komanso kukukuta mano ndipo amafooka. Ndinapempha ophunzira anu kuti autulutse koma alephera.”
-