Maliko 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Aliyense amene walandira mwana wamngʼono+ ngati ameneyu mʼdzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense amene walandira ine, sanalandire ine ndekha, koma walandiranso Mulungu amene anandituma.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:37 Yesu—Ndi Njira, tsa. 149 Nsanja ya Olonda,2/1/2007, ptsa. 9-10
37 “Aliyense amene walandira mwana wamngʼono+ ngati ameneyu mʼdzina langa, walandiranso ine. Ndipo aliyense amene walandira ine, sanalandire ine ndekha, koma walandiranso Mulungu amene anandituma.”+