Maliko 10:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndiyeno Yesu anamufunsa kuti: “Ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?” Munthu amene anali ndi vuto losaonayo anayankha kuti: “Rab·boʹni,* ndithandizeni kuti ndiyambe kuona.”
51 Ndiyeno Yesu anamufunsa kuti: “Ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?” Munthu amene anali ndi vuto losaonayo anayankha kuti: “Rab·boʹni,* ndithandizeni kuti ndiyambe kuona.”