Maliko 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo atayandikira ku Yerusalemu, ku Betefage ndi ku Betaniya+ paphiri la Maolivi, Yesu anatumiza ophunzira ake awiri.+
11 Iwo atayandikira ku Yerusalemu, ku Betefage ndi ku Betaniya+ paphiri la Maolivi, Yesu anatumiza ophunzira ake awiri.+