Maliko 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kunena zoona, Yehova* akanapanda kufupikitsa masikuwo, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwa amene iye anawasankha, wafupikitsa masikuwo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:20 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, tsa. 10
20 Kunena zoona, Yehova* akanapanda kufupikitsa masikuwo, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwa amene iye anawasankha, wafupikitsa masikuwo.+