Maliko 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano phunzirani zokhudza mtengo wa mkuyu kuchokera pa fanizo ili: Nthambi yake yanthete ikaphuka nʼkuchita masamba, mumadziwa kuti chilimwe chili pafupi.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:28 Yesu—Ndi Njira, tsa. 258 Nsanja ya Olonda,4/1/1990, tsa. 25
28 Tsopano phunzirani zokhudza mtengo wa mkuyu kuchokera pa fanizo ili: Nthambi yake yanthete ikaphuka nʼkuchita masamba, mumadziwa kuti chilimwe chili pafupi.+