Maliko 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Akupitiriza kudya, iye anatenga mkate nʼkuyamika Mulungu. Kenako anaunyemanyema nʼkuwapatsa ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:22 Nsanja ya Olonda,1/15/1991, tsa. 212/15/1990, ptsa. 16-17
22 Akupitiriza kudya, iye anatenga mkate nʼkuyamika Mulungu. Kenako anaunyemanyema nʼkuwapatsa ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+