Maliko 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chimodzimodzinso ansembe aakulu limodzi ndi alembi nawonso ankamunyoza. Iwo ankanena kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika!+
31 Chimodzimodzinso ansembe aakulu limodzi ndi alembi nawonso ankamunyoza. Iwo ankanena kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika!+