Maliko 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya mayi wa Yose, anapitiriza kuyangʼanitsitsa pamene anaikidwapo.+
47 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya mayi wa Yose, anapitiriza kuyangʼanitsitsa pamene anaikidwapo.+