Maliko 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmawa kwambiri tsiku loyamba la mlunguwo, iwo anafika kumandawo* dzuwa litatuluka.+