Luka 1:76 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 76 Koma kunena za mwana wamngʼonowe, udzatchedwa mneneri wa Wamʼmwambamwamba, chifukwa udzatsogola pamaso pa Yehova* kuti ukakonze njira zake.+ 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Ulosi wa Zekariya (gnj 1 27:15–30:56)
76 Koma kunena za mwana wamngʼonowe, udzatchedwa mneneri wa Wamʼmwambamwamba, chifukwa udzatsogola pamaso pa Yehova* kuti ukakonze njira zake.+