Luka 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi, nkhwangwa yaikidwa kale pamizu ya mitengo. Choncho mtengo uliwonse wosabereka zipatso zabwino udulidwa nʼkuponyedwa pamoto.”+
9 Ndithudi, nkhwangwa yaikidwa kale pamizu ya mitengo. Choncho mtengo uliwonse wosabereka zipatso zabwino udulidwa nʼkuponyedwa pamoto.”+