Luka 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthawi inayake, gulu la anthu linkamvetsera pamene Yesu ankaphunzitsa mawu a Mulungu mʼmphepete mwa nyanja ya Genesarete*+ ndipo anthuwo ankamupanikiza.
5 Nthawi inayake, gulu la anthu linkamvetsera pamene Yesu ankaphunzitsa mawu a Mulungu mʼmphepete mwa nyanja ya Genesarete*+ ndipo anthuwo ankamupanikiza.