Luka 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atachita zimenezo, anagwira nsomba zochuluka kwambiri. Ndipo maukonde awo anayamba kungʼambika.+