-
Luka 5:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho anakodola anzawo amene anali mʼngalawa ina kuti adzawathandize. Iwo anabweradi, ndipo nsombazo zinadzaza ngalawa zonse ziwiri, moti ngalawazo zinayamba kumira.
-