Luka 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi inanso pamene anali mumzinda wina, anakumana ndi munthu wakhate thupi lonse. Munthuyo ataona Yesu, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anamupempha kuti: “Ambuye, ndikudziwa kuti ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:12 “Wotsatira Wanga,” tsa. 142 Nsanja ya Olonda,6/15/2015, tsa. 911/1/1994, ptsa. 12-1311/15/1989, tsa. 244/15/1986, ptsa. 8-9 Yesu—Ndi Njira, tsa. 65
12 Nthawi inanso pamene anali mumzinda wina, anakumana ndi munthu wakhate thupi lonse. Munthuyo ataona Yesu, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anamupempha kuti: “Ambuye, ndikudziwa kuti ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+
5:12 “Wotsatira Wanga,” tsa. 142 Nsanja ya Olonda,6/15/2015, tsa. 911/1/1994, ptsa. 12-1311/15/1989, tsa. 244/15/1986, ptsa. 8-9 Yesu—Ndi Njira, tsa. 65