Luka 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense. Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe, ndipo ukapereke nsembe ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira,+ kuti ikhale umboni kwa iwo.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 65 Nsanja ya Olonda,4/15/1986, tsa. 9
14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense. Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe, ndipo ukapereke nsembe ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira,+ kuti ikhale umboni kwa iwo.”+