-
Luka 5:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma atalephera kudutsa naye chifukwa cha kuchuluka kwa anthu, anakwera padenga. Ndipo kudzera pabowo limene anapanga padengapo, anamutsitsa limodzi ndi machirawo nʼkumufikitsa pakati pa anthu amene anali pamaso pa Yesu.
-