-
Luka 5:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Komanso palibe amene amathira vinyo watsopano mʼmatumba achikopa akale. Munthu akachita zimenezo, vinyo watsopanoyo amaphulitsa matumba achikopawo ndipo amatayika. Ndiponso matumba achikopawo amawonongeka.
-