-
Luka 6:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ngati mumachitira zabwino okhawo amene amakuchitirani zabwino, mudzapindula chiyani? Chifukwa ngakhale ochimwa amachita zomwezo.
-