Luka 6:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pamene munthu amene wamva koma osachita chilichonse,+ ali ngati munthu amene wamanga nyumba yopanda maziko padothi. Apanso mtsinje unasefukira nʼkuwomba nyumbayo, ndipo nthawi yomweyo inagwa, moti kugwa kwake kunali kwakukulu.”
49 Pamene munthu amene wamva koma osachita chilichonse,+ ali ngati munthu amene wamanga nyumba yopanda maziko padothi. Apanso mtsinje unasefukira nʼkuwomba nyumbayo, ndipo nthawi yomweyo inagwa, moti kugwa kwake kunali kwakukulu.”