-
Luka 7:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nʼchifukwa chake inenso sindinadzione kuti ndine woyenera kubwera kwa inu. Koma mungonena mawu okha ndipo wantchito wangayo achira.
-