-
Luka 7:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Chifukwa inenso ndili ndi akuluakulu amene anaikidwa kuti azindiyangʼanira komanso ndili ndi asilikali amene ndimawayangʼanira. Ndikauza mmodzi kuti, ‘Pita!’ amapita, wina ndikamuuza kuti, ‘Bwera!’ amabwera. Kapolo wanga ndikamuuza kuti, ‘Chita ichi!’ amachita.”
-