Luka 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nanga munapita kukaona chiyani? Munthu wovala zovala zapamwamba kapena?+ Ayi, paja amene amavala zovala zapamwamba ndiponso anthu amene amakhala moyo wamwanaalirenji amapezeka mʼnyumba zachifumu.
25 Nanga munapita kukaona chiyani? Munthu wovala zovala zapamwamba kapena?+ Ayi, paja amene amavala zovala zapamwamba ndiponso anthu amene amakhala moyo wamwanaalirenji amapezeka mʼnyumba zachifumu.