Luka 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mwana wa munthu wabwera ndipo iye akudya ndi kumwa, koma inu mukunena kuti: ‘Taonani! Munthu wosusuka ndi wokonda kwambiri vinyo, bwenzi la okhometsa msonkho ndi ochimwa!’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:34 Yesu—Ndi Njira, tsa. 98 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 24
34 Mwana wa munthu wabwera ndipo iye akudya ndi kumwa, koma inu mukunena kuti: ‘Taonani! Munthu wosusuka ndi wokonda kwambiri vinyo, bwenzi la okhometsa msonkho ndi ochimwa!’+