Luka 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe amene amati akayatsa nyale, amaivindikira ndi chiwiya kapena kuiika pansi pa bedi. Koma amaiika pachoikapo nyale kuti amene akulowa aone kuwala.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:16 Nsanja ya Olonda,4/1/1987, tsa. 8
16 Palibe amene amati akayatsa nyale, amaivindikira ndi chiwiya kapena kuiika pansi pa bedi. Koma amaiika pachoikapo nyale kuti amene akulowa aone kuwala.+