Luka 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha Yesu anawauza kuti: “Mayi anga ndi azichimwene anga ndi awa amene amamvetsera mawu a Mulungu nʼkumawachita.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 105 Nsanja ya Olonda,8/15/1987, tsa. 8
21 Poyankha Yesu anawauza kuti: “Mayi anga ndi azichimwene anga ndi awa amene amamvetsera mawu a Mulungu nʼkumawachita.”+