Luka 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ulendowo uli mkati, Yesu anagona tulo. Kenako panyanjapo panayamba kuwomba mphepo yamkuntho, ndipo madzi anayamba kudzaza mʼngalawamo moti akanatha kumira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:23 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113 Nsanja ya Olonda,5/1/1987, tsa. 8
23 Koma ulendowo uli mkati, Yesu anagona tulo. Kenako panyanjapo panayamba kuwomba mphepo yamkuntho, ndipo madzi anayamba kudzaza mʼngalawamo moti akanatha kumira.+