Luka 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anapita kukamudzutsa ndipo anamuuza kuti: “Mlangizi, Mlangizi, tikufa!” Atamva zimenezi anadzuka nʼkudzudzula mphepo ndi mafunde amphamvuwo, moti zinasiya, ndipo panyanjapo panakhala bata.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113
24 Kenako anapita kukamudzutsa ndipo anamuuza kuti: “Mlangizi, Mlangizi, tikufa!” Atamva zimenezi anadzuka nʼkudzudzula mphepo ndi mafunde amphamvuwo, moti zinasiya, ndipo panyanjapo panakhala bata.+