Luka 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno anaimika ngalawa ija mʼdera la Agerasa,+ tsidya linalo, moyangʼanizana ndi Galileya.