Luka 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno munthu amene anamutulutsa ziwanda uja anamupempha mobwerezabwereza kuti aziyenda naye. Koma Yesu anauza munthuyo kuti apite kwawo. Iye anati:+
38 Ndiyeno munthu amene anamutulutsa ziwanda uja anamupempha mobwerezabwereza kuti aziyenda naye. Koma Yesu anauza munthuyo kuti apite kwawo. Iye anati:+